Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 7:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Kenako Solomo anamanga nyumba yake yokhalamo kubwalo lina+ chapatali ndi nyumba ya Bwalo la Mpando Wachifumu. Kamangidwe ka nyumbayi kanali kofanana ndi ka Bwalo la Mpando Wachifumu. Panalinso nyumba ina yofanana ndi Bwaloli imene Solomo anamangira mwana wamkazi wa Farao+ amene iye anam’kwatira.

  • 1 Mafumu 9:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Solomo anamanganso Gezeri, Beti-horoni Wakumunsi,+

  • 2 Mbiri 9:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Mfumu Solomo inapanga zishango 200 zikuluzikulu zagolide wosakaniza ndi zitsulo zina.+ (Chishango chachikulu chilichonse anachikuta ndi golide wosakaniza ndi zitsulo zina wolemera masekeli 600.)+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena