Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kenako Solomo anachita mgwirizano wa ukwati+ ndi Farao mfumu ya Iguputo. Anatenga mwana wamkazi wa Faraoyo+ n’kubwera naye ku Mzinda wa Davide,+ kuti azikhala kaye kumeneko mpaka iye atamaliza kumanga nyumba yake,+ nyumba ya Yehova,+ ndi mpanda wozungulira Yerusalemu yense.+

  • 1 Mafumu 9:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Mwana wamkazi wa Farao+ anachoka ku Mzinda wa Davide+ n’kukakhala kunyumba yake imene Solomo anam’mangira. Panali pa nthawi imeneyi pamene Solomo anamanga Chimulu cha Dothi.*+

  • 2 Mbiri 8:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Solomo anatulutsa mwana wamkazi wa Farao+ mu Mzinda wa Davide+ n’kukamuika m’nyumba imene anam’mangira,+ pakuti iye anati: “Ngakhale ali mkazi wanga, asamakhale m’nyumba ya Davide mfumu ya Isiraeli, chifukwa malo alionse amene likasa la Yehova likukhala ndi oyera.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena