Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kenako Solomo anachita mgwirizano wa ukwati+ ndi Farao mfumu ya Iguputo. Anatenga mwana wamkazi wa Faraoyo+ n’kubwera naye ku Mzinda wa Davide,+ kuti azikhala kaye kumeneko mpaka iye atamaliza kumanga nyumba yake,+ nyumba ya Yehova,+ ndi mpanda wozungulira Yerusalemu yense.+

  • 1 Mafumu 7:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Kenako Solomo anamanga nyumba yake yokhalamo kubwalo lina+ chapatali ndi nyumba ya Bwalo la Mpando Wachifumu. Kamangidwe ka nyumbayi kanali kofanana ndi ka Bwalo la Mpando Wachifumu. Panalinso nyumba ina yofanana ndi Bwaloli imene Solomo anamangira mwana wamkazi wa Farao+ amene iye anam’kwatira.

  • 2 Mbiri 8:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Solomo anatulutsa mwana wamkazi wa Farao+ mu Mzinda wa Davide+ n’kukamuika m’nyumba imene anam’mangira,+ pakuti iye anati: “Ngakhale ali mkazi wanga, asamakhale m’nyumba ya Davide mfumu ya Isiraeli, chifukwa malo alionse amene likasa la Yehova likukhala ndi oyera.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena