14 Ndipulumutseni kwa anthu ndi dzanja lanu, inu Yehova,+
Ndipulumutseni kwa anthu a m’nthawi ino,+ amene gawo lawo lili m’moyo uno.+
Anthu amene mimba zawo mwazidzaza ndi chuma chanu chobisika,+
Amene ali ndi ana aamuna ochuluka,+
Ndipo amakundikira ana awo chuma.+