Mlaliki 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti nzeru zikachuluka pamachulukanso kukhumudwa,+ choncho amene amadziwa zinthu zambiri amakhalanso ndi zopweteka zambiri.+ Machitidwe 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndithudi, ambiri ndithu amene anali kuchita zamatsenga+ anasonkhanitsa mabuku awo pamodzi ndi kuwatentha pamaso pa onse. Ndipo atawonkhetsa mitengo yake, anapeza ndalama zasiliva zokwana 50,000. Akolose 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Samalani: mwina wina angakugwireni+ ngati nyama, mwa nzeru za anthu+ ndi chinyengo chopanda pake,+ malinga ndi miyambo ya anthu, malinganso ndi mfundo zimene zili maziko a moyo wa m’dzikoli,+ osati malinga ndi Khristu,
18 Pakuti nzeru zikachuluka pamachulukanso kukhumudwa,+ choncho amene amadziwa zinthu zambiri amakhalanso ndi zopweteka zambiri.+
19 Ndithudi, ambiri ndithu amene anali kuchita zamatsenga+ anasonkhanitsa mabuku awo pamodzi ndi kuwatentha pamaso pa onse. Ndipo atawonkhetsa mitengo yake, anapeza ndalama zasiliva zokwana 50,000.
8 Samalani: mwina wina angakugwireni+ ngati nyama, mwa nzeru za anthu+ ndi chinyengo chopanda pake,+ malinga ndi miyambo ya anthu, malinganso ndi mfundo zimene zili maziko a moyo wa m’dzikoli,+ osati malinga ndi Khristu,