Deuteronomo 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakati panu pasapezeke munthu wotentha mwana wake pamoto,*+ wolosera,+ wochita zamatsenga,+ woombeza,*+ wanyanga,+ Danieli 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo mfumuyo inalamula kuti aitane ansembe onse ochita zamatsenga,+ anthu olankhula ndi mizimu, Akasidi* ndi anthu ena ochita zamatsenga kuti adzauze mfumu maloto akewo.+ Anthu amenewa anafika ndi kuima pamaso pa mfumu. Machitidwe 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano mumzindawo munalinso munthu wina dzina lake Simoni. Izi zisanachitike, iyeyu anali kuchita zamatsenga+ ndi kudabwitsa anthu onse mu Samariya. Anali kudzitamandira kuti anali wopambana.+
10 Pakati panu pasapezeke munthu wotentha mwana wake pamoto,*+ wolosera,+ wochita zamatsenga,+ woombeza,*+ wanyanga,+
2 Pamenepo mfumuyo inalamula kuti aitane ansembe onse ochita zamatsenga,+ anthu olankhula ndi mizimu, Akasidi* ndi anthu ena ochita zamatsenga kuti adzauze mfumu maloto akewo.+ Anthu amenewa anafika ndi kuima pamaso pa mfumu.
9 Tsopano mumzindawo munalinso munthu wina dzina lake Simoni. Izi zisanachitike, iyeyu anali kuchita zamatsenga+ ndi kudabwitsa anthu onse mu Samariya. Anali kudzitamandira kuti anali wopambana.+