Miyambo 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Maso ako aziyang’ana patsogolo.+ Maso ako owala aziyang’anitsitsa patsogolo pako.+ Miyambo 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nzeru za munthu wochenjera ndizo kuzindikira njira imene akuyendamo,+ koma kuganiza mopusa kwa zitsiru ndi chinyengo.+ Miyambo 23:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mwana wanga, ndipatse mtima wako, ndipo maso ako asangalale ndi njira zanga.+
8 Nzeru za munthu wochenjera ndizo kuzindikira njira imene akuyendamo,+ koma kuganiza mopusa kwa zitsiru ndi chinyengo.+