Yoswa 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano Yoswa anauza anthu onse kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Kalekale, makolo anu,+ kuphatikizapo Tera, bambo ake a Abulahamu ndi Nahori,+ ankakhala kutsidya lina la Mtsinje,*+ ndipo ankatumikira milungu ina.
2 Tsopano Yoswa anauza anthu onse kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Kalekale, makolo anu,+ kuphatikizapo Tera, bambo ake a Abulahamu ndi Nahori,+ ankakhala kutsidya lina la Mtsinje,*+ ndipo ankatumikira milungu ina.