Salimo 44:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pakuti miyoyo yathu yasautsika.+Mimba zathu zili thasa! padothi. Yesaya 51:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndidzachiika m’manja mwa amene akukuvutitsa,+ amene akukuuza kuti, ‘Werama kuti tiwolokere pamsana pako,’ amene akuona msana wako ngati pansi popondapo, ndiponso ngati njira yowolokerapo.”+
23 Ndidzachiika m’manja mwa amene akukuvutitsa,+ amene akukuuza kuti, ‘Werama kuti tiwolokere pamsana pako,’ amene akuona msana wako ngati pansi popondapo, ndiponso ngati njira yowolokerapo.”+