Nehemiya 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu Mulungu wanga, kumbukirani+ zinthu zonse zimene Tobia+ ndi Sanibalati anachita. Mukumbukirenso Nowadiya mneneri wamkazi+ ndi aneneri ena onse amene anali kuyesetsabe kundiopseza. Yesaya 49:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma Yehova wanena kuti: “Ngakhale gulu la anthu ogwidwa ndi munthu wamphamvu lidzatengedwa,+ ndipo amene anatengedwa kale ndi wolamulira wankhanza adzathawa.+ Aliyense wolimbana nawe, ineyo ndidzalimbana naye,+ ndipo ana ako ndidzawapulumutsa.+
14 Inu Mulungu wanga, kumbukirani+ zinthu zonse zimene Tobia+ ndi Sanibalati anachita. Mukumbukirenso Nowadiya mneneri wamkazi+ ndi aneneri ena onse amene anali kuyesetsabe kundiopseza.
25 Koma Yehova wanena kuti: “Ngakhale gulu la anthu ogwidwa ndi munthu wamphamvu lidzatengedwa,+ ndipo amene anatengedwa kale ndi wolamulira wankhanza adzathawa.+ Aliyense wolimbana nawe, ineyo ndidzalimbana naye,+ ndipo ana ako ndidzawapulumutsa.+