Yesaya 33:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti Yehova ndiye Woweruza wathu.+ Yehova ndiye Wotipatsa Malamulo.+ Yehova ndiye Mfumu yathu.+ Iye adzatipulumutsa.+
22 Pakuti Yehova ndiye Woweruza wathu.+ Yehova ndiye Wotipatsa Malamulo.+ Yehova ndiye Mfumu yathu.+ Iye adzatipulumutsa.+