Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 10:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 “M’tsiku limenelo, katundu wake adzachoka paphewa panu,+ ndipo goli lake lidzachoka m’khosi mwanu.+ Golilo lidzathyoledwa+ chifukwa cha mafuta.”

  • Yesaya 52:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Dzuka pafumbi pamene ulipo.+ Sansa fumbilo, khala pamalo aulemu iwe Yerusalemu. Masula zingwe zimene zili m’khosi mwako, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni wogwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina.+

  • Yeremiya 29:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Yehova wanena kuti, ‘Zaka 70 zikadzakwanira muli ku Babulo ndidzakucheukirani anthu inu,+ ndipo ndidzakwaniritsa lonjezo langa lokubwezeretsani kumalo ano.’+

  • Yeremiya 50:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Wowawombola ndi wamphamvu,+ dzina lake ndi Yehova wa makamu.+ Iye sadzalephera kuwaweruzira mlandu wawo+ kuti apumitse dziko lawo+ ndiponso kusokoneza mtendere wa anthu okhala m’Babulo.”+

  • Zekariya 9:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Koma mkazi iwe, chifukwa cha magazi a pangano limene unapangana ndi ine,+ ndidzatulutsa akaidi ako+ m’dzenje lopanda madzi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena