Yeremiya 50:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Koma Wowawombola ndi wamphamvu.+ Dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.+ Iye sadzalephera kuwaweruzira mlandu wawo,+Kuti abweretse mtendere mʼdziko lawo+Ndi kusokoneza mtendere wa anthu okhala mʼBabulo.”+
34 Koma Wowawombola ndi wamphamvu.+ Dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.+ Iye sadzalephera kuwaweruzira mlandu wawo,+Kuti abweretse mtendere mʼdziko lawo+Ndi kusokoneza mtendere wa anthu okhala mʼBabulo.”+