Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 26:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Pakuti iye watsitsa anthu okhala pamalo okwezeka,+ okhala m’mudzi wokwezeka.+ Mudziwo wautsitsa. Wautsitsira pansi, waugwetsa mpaka pafumbi.+

  • Yeremiya 51:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Thawani ndi kutuluka m’Babulo+ ndipo aliyense apulumutse moyo wake.+ Musawonongeke chifukwa cha zolakwa zake.+ Ino ndi nthawi yoti Yehova amubwezere chilango.+ Mulungu abwezera Babulo mogwirizana ndi zochita zake.+

  • Zekariya 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Fulumirani! Fulumirani anthu inu! Thawani m’dziko la kumpoto,”+ watero Yehova.

      “Anthu inu, ndinakubalalitsirani kutali kumbali zonse za dziko lapansi,”*+ watero Yehova.

  • Chivumbulutso 18:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndipo ndinamva mawu ena kumwamba, akuti: “Tulukani mwa iye anthu anga,+ ngati simukufuna kugawana naye machimo ake,+ ndiponso ngati simukufuna kulandira nawo ina ya miliri yake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena