Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 31:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 “Taonani! Masiku adzafika, pamene ndidzachita pangano latsopano+ ndi nyumba ya Isiraeli+ komanso ndi nyumba ya Yuda,”+ watero Yehova.

  • Mateyu 26:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Vinyoyu akuimira+ ‘magazi+ anga a pangano,’+ amene adzakhetsedwa chifukwa cha anthu ambiri+ kuti machimo akhululukidwe.+

  • Aheberi 12:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Kulinso Yesu, mkhalapakati+ wa pangano latsopano,+ ndiponso magazi owaza,+ amene amalankhula m’njira yabwino kwambiri kuposa magazi a Abele.+

  • Aheberi 13:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Tsopano, Mulungu wamtendere,+ amene anaukitsa kwa akufa+ m’busa wamkulu+ wa nkhosa+ wokhala ndi magazi a pangano losatha,+ Ambuye wathu Yesu,

  • 1 Petulo 1:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Koma munamasulidwa ndi magazi amtengo wapatali,+ monga a nkhosa yopanda chilema ndi yopanda mawanga,+ magazi a Khristu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena