Salimo 35:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Weruzani mlandu wanga inu Yehova, motsutsana ndi adani anga.+Menyani nkhondo ndi kugonjetsa amene akumenyana ndi ine.+ Salimo 43:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Ndiweruzeni+ inu Mulungu,Weruzani mlandu wanga+ motsutsana ndi mtundu wosakhulupirika.Ndipulumutseni kwa munthu wachinyengo ndi wochita zosalungama.+ Maliro 3:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Inu Yehova, mwaona zoipa zimene andichitira.+ Chonde, ndiweruzireni mlandu wanga.+
35 Weruzani mlandu wanga inu Yehova, motsutsana ndi adani anga.+Menyani nkhondo ndi kugonjetsa amene akumenyana ndi ine.+
43 Ndiweruzeni+ inu Mulungu,Weruzani mlandu wanga+ motsutsana ndi mtundu wosakhulupirika.Ndipulumutseni kwa munthu wachinyengo ndi wochita zosalungama.+