Yeremiya 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsoka ine,+ chifukwa inu mayi anga munabereka ine munthu amene nthawi zonse ndimakangana ndipo ndimalimbana ndi dziko lonse.+ Sindinapereke ngongole komanso sanandikongoze kalikonse, koma anthu onse akunditemberera.+
10 Tsoka ine,+ chifukwa inu mayi anga munabereka ine munthu amene nthawi zonse ndimakangana ndipo ndimalimbana ndi dziko lonse.+ Sindinapereke ngongole komanso sanandikongoze kalikonse, koma anthu onse akunditemberera.+