Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 25:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Ndiyeno Davide anamva kuti Nabala wamwalira. Atatero, iye anati: “Adalitsike Yehova amene wandiweruzira mlandu+ ndi kundimasula ku chitonzo+ cha Nabala, komanso wagwira ine mtumiki wake kuti ndisachite choipa.+ Yehova wabwezera zoipa za Nabala pamutu pake!”+ Pamenepo Davide anatumiza anthu kuti akamufunsirire Abigayeli, kuti akhale mkazi wake.+

  • Salimo 9:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Chifukwa mwandiweruzira mlandu wanga ndi dandaulo langa.+

      Mwakhala pampando wachifumu ndipo mukuweruza mwachilungamo.+

  • Salimo 35:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Nyamukani ndi kukhala maso kuti mundichitire chilungamo,+

      Chitani zimenezi inu Mulungu wanga Yehova, kuti muweruze mlandu wanga.+

  • Salimo 43:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Ndiweruzeni+ inu Mulungu,

      Weruzani mlandu wanga+ motsutsana ndi mtundu wosakhulupirika.

      Ndipulumutseni kwa munthu wachinyengo ndi wochita zosalungama.+

  • Yeremiya 51:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Choncho Yehova wanena kuti: “Ine ndikukuyankhira mlandu,+ ndipo ndidzakubwezerera chilango.+ Ndidzaphwetsa nyanja yake ndi zitsime zake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena