Yesaya 32:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 kufikira mzimu utatsanulidwa pa ife kuchokera kumwamba,+ ndiponso chipululu chitakhala munda wa zipatso. Munda wa zipatsowo udzakhala ngati nkhalango yeniyeni.+
15 kufikira mzimu utatsanulidwa pa ife kuchokera kumwamba,+ ndiponso chipululu chitakhala munda wa zipatso. Munda wa zipatsowo udzakhala ngati nkhalango yeniyeni.+