Salimo 104:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mukatumiza mzimu wanu zimalengedwa.+Ndipo mumachititsa dziko kukhala latsopano. Miyambo 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mverani kudzudzula kwanga ndipo mubwerere.+ Mukatero ndidzachititsa kuti mzimu wanga usefukire kwa inu+ ndipo ndidzakudziwitsani mawu anga.+ Yesaya 44:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ndidzapatsa madzi munthu waludzu,+ ndipo ndidzaika timitsinje tamadzi pamalo ouma.+ Ndidzatsanulira mzimu wanga pambewu yako+ ndi madalitso anga pa mbadwa zako.
23 Mverani kudzudzula kwanga ndipo mubwerere.+ Mukatero ndidzachititsa kuti mzimu wanga usefukire kwa inu+ ndipo ndidzakudziwitsani mawu anga.+
3 Pakuti ndidzapatsa madzi munthu waludzu,+ ndipo ndidzaika timitsinje tamadzi pamalo ouma.+ Ndidzatsanulira mzimu wanga pambewu yako+ ndi madalitso anga pa mbadwa zako.