Yesaya 36:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ukudalira thandizo la Iguputo,+ bango lophwanyika loti munthu ataligwira kuti limuchirikize,+ lingamucheke m’manja. Umu ndi mmene Farao+ mfumu ya Iguputo alili kwa onse omudalira.+
6 Ukudalira thandizo la Iguputo,+ bango lophwanyika loti munthu ataligwira kuti limuchirikize,+ lingamucheke m’manja. Umu ndi mmene Farao+ mfumu ya Iguputo alili kwa onse omudalira.+