Yesaya 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Aiguputowo ndi anthu ochokera kufumbi.+ Si Mulungu ayi. Mahatchi awo ndi zinyama,+ osati mzimu. Yehova akadzatambasula dzanja lake, amene akupereka thandizo adzapunthwa, ndipo amene akuthandizidwawo adzagwa.+ Onsewo adzatha nthawi imodzi. Yeremiya 2:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 N’chifukwa chiyani kusintha njira kwako ukukuona mopepuka?+ Udzachitanso manyazi ndi Iguputo+ monga mmene unachitira manyazi ndi Asuri.+ Hoseya 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Efuraimu anaona kudwala kwake ndipo Yuda anaona chilonda chake.+ Pamenepo Efuraimu anapita ku Asuri+ ndipo anatumiza amithenga kwa mfumu yaikulu.+ Koma mfumuyo sinathe kukuchiritsani anthu inu,+ ndipo sinathe kupoletsa chilonda chanu.+
3 Koma Aiguputowo ndi anthu ochokera kufumbi.+ Si Mulungu ayi. Mahatchi awo ndi zinyama,+ osati mzimu. Yehova akadzatambasula dzanja lake, amene akupereka thandizo adzapunthwa, ndipo amene akuthandizidwawo adzagwa.+ Onsewo adzatha nthawi imodzi.
36 N’chifukwa chiyani kusintha njira kwako ukukuona mopepuka?+ Udzachitanso manyazi ndi Iguputo+ monga mmene unachitira manyazi ndi Asuri.+
13 “Efuraimu anaona kudwala kwake ndipo Yuda anaona chilonda chake.+ Pamenepo Efuraimu anapita ku Asuri+ ndipo anatumiza amithenga kwa mfumu yaikulu.+ Koma mfumuyo sinathe kukuchiritsani anthu inu,+ ndipo sinathe kupoletsa chilonda chanu.+