Yesaya 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Lidzafikiranso nsanja iliyonse yaitali ndi khoma* lililonse lolimba kwambiri.+ Yesaya 32:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti nsanja yokhalamo yasiyidwa,+ piringupiringu amene anali mumzindamo watha. Ofeli+ ndi nsanja ya mlonda zasanduka tchire. Mpaka kalekale zidzakhala malo osangalalako mbidzi, ndi odyetserako ziweto,
14 Pakuti nsanja yokhalamo yasiyidwa,+ piringupiringu amene anali mumzindamo watha. Ofeli+ ndi nsanja ya mlonda zasanduka tchire. Mpaka kalekale zidzakhala malo osangalalako mbidzi, ndi odyetserako ziweto,