Yesaya 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 ndipo idzadutsa mu Yuda yense. Idzadutsa ngati madzi osefukira,+ ndipo idzafika mpaka m’khosi.+ Idzatambasula mapiko ake+ mpaka m’lifupi mwa dziko lako, iwe Emanueli.”+
8 ndipo idzadutsa mu Yuda yense. Idzadutsa ngati madzi osefukira,+ ndipo idzafika mpaka m’khosi.+ Idzatambasula mapiko ake+ mpaka m’lifupi mwa dziko lako, iwe Emanueli.”+