Deuteronomo 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma asadzichulukitsire mahatchi+ kapena kuchititsa anthu kubwerera ku Iguputo kuti akakhale ndi mahatchi ochuluka+ pakuti Yehova wakuuzani kuti, ‘Musabwererenso kudzera njira iyi.’ Salimo 33:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Hatchi siingabweretse chipulumutso,+Siingapulumutse munthu chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake.+ Miyambo 21:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Hatchi* anaikonzera tsiku la nkhondo,+ koma Yehova ndiye amapulumutsa.+
16 Koma asadzichulukitsire mahatchi+ kapena kuchititsa anthu kubwerera ku Iguputo kuti akakhale ndi mahatchi ochuluka+ pakuti Yehova wakuuzani kuti, ‘Musabwererenso kudzera njira iyi.’
17 Hatchi siingabweretse chipulumutso,+Siingapulumutse munthu chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake.+