Nahumu 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ngakhale kuti iwo alukanalukana ngati minga+ ndipo aledzera ngati kuti amwa mowa,+ adzatenthedwa ngati mapesi ouma.+
10 Ngakhale kuti iwo alukanalukana ngati minga+ ndipo aledzera ngati kuti amwa mowa,+ adzatenthedwa ngati mapesi ouma.+