Yesaya 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chifukwa cha mkwiyo wa Yehova wa makamu, dzikolo layaka moto ndipo anthu adzakhala ngati chakudya cha motowo.+ Palibe amene adzamvere chisoni aliyense, ngakhale m’bale wake.+ Yesaya 33:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu inu muli ndi pakati pa udzu wouma+ ndipo mudzabereka mapesi. Mzimu wanu udzakunyeketsani+ ngati moto.+ Malaki 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Taonani! Tsiku loyaka ngati ng’anjo likubwera,+ ndipo anthu onse odzikuza ndi onse ochita zoipa adzakhala ngati mapesi.+ Tsiku limene likubweralo lidzawanyeketsa moti pa iwo sipadzatsala mizu kapena nthambi,”+ watero Yehova wa makamu.
19 Chifukwa cha mkwiyo wa Yehova wa makamu, dzikolo layaka moto ndipo anthu adzakhala ngati chakudya cha motowo.+ Palibe amene adzamvere chisoni aliyense, ngakhale m’bale wake.+
11 Anthu inu muli ndi pakati pa udzu wouma+ ndipo mudzabereka mapesi. Mzimu wanu udzakunyeketsani+ ngati moto.+
4 “Taonani! Tsiku loyaka ngati ng’anjo likubwera,+ ndipo anthu onse odzikuza ndi onse ochita zoipa adzakhala ngati mapesi.+ Tsiku limene likubweralo lidzawanyeketsa moti pa iwo sipadzatsala mizu kapena nthambi,”+ watero Yehova wa makamu.