Salimo 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo ndi za Yehova,+Nthaka ndi yake pamodzi ndi onse okhala panthakapo.+
24 Dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo ndi za Yehova,+Nthaka ndi yake pamodzi ndi onse okhala panthakapo.+