Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 11:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Akhungu akuonanso,+ olumala+ akuyendayenda, akhate+ akuyeretsedwa ndipo ogontha+ akumva. Akufa+ akuukitsidwa, ndipo kwa aumphawi uthenga wabwino ukulengezedwa.+

  • Mateyu 21:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Anthu akhungu ndi olumala anabwera kwa iye m’kachisimo, ndipo anawachiritsa.

  • Machitidwe 8:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kumeneko kunali anthu ambiri ogwidwa ndi mizimu yonyansa,+ ndipo inali kufuula mokweza mawu ndi kutuluka. Ndipo anthu ambiri amene anali akufa ziwalo+ ndi olumala anali kuchiritsidwa.

  • Machitidwe 14:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Choncho Paulo analankhula mokweza mawu kuti: “Imirira ndi miyendo yako!” Pamenepo iye anadumpha n’kuyamba kuyenda.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena