Yesaya 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano Yehova anauza Yesaya kuti: “Pita ukakumane ndi Ahazi. Upite ndi mwana wako Seari-yasubu.*+ Ukakumane ndi Ahaziyo pamapeto pa ngalande+ yochokera kudziwe lakumtunda, m’mphepete mwa msewu waukulu wopita kumalo a wochapa zovala.+
3 Tsopano Yehova anauza Yesaya kuti: “Pita ukakumane ndi Ahazi. Upite ndi mwana wako Seari-yasubu.*+ Ukakumane ndi Ahaziyo pamapeto pa ngalande+ yochokera kudziwe lakumtunda, m’mphepete mwa msewu waukulu wopita kumalo a wochapa zovala.+