Salimo 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nyamukani, inu Yehova, yang’anizanani naye maso ndi maso woipayo.+M’gonjetseni. Pulumutsani moyo wanga kwa woipayo ndi lupanga lanu.+ Yesaya 55:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 ndi mmenenso adzakhalire mawu otuluka pakamwa panga.+ Sadzabwerera kwa ine popanda kukwaniritsa cholinga chake,+ koma adzachitadi zimene ine ndikufuna+ ndipo adzakwaniritsadi zimene ndinawatumizira.+
13 Nyamukani, inu Yehova, yang’anizanani naye maso ndi maso woipayo.+M’gonjetseni. Pulumutsani moyo wanga kwa woipayo ndi lupanga lanu.+ Yesaya 55:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 ndi mmenenso adzakhalire mawu otuluka pakamwa panga.+ Sadzabwerera kwa ine popanda kukwaniritsa cholinga chake,+ koma adzachitadi zimene ine ndikufuna+ ndipo adzakwaniritsadi zimene ndinawatumizira.+
11 ndi mmenenso adzakhalire mawu otuluka pakamwa panga.+ Sadzabwerera kwa ine popanda kukwaniritsa cholinga chake,+ koma adzachitadi zimene ine ndikufuna+ ndipo adzakwaniritsadi zimene ndinawatumizira.+