Ekisodo 38:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako anapanga beseni losambira lamkuwa+ ndi choikapo chake chamkuwa. Popanga zimenezi anagwiritsa ntchito akalirole* a akazi otumikira, amene anali kutumikira mwadongosolo pachipata cha chihema chokumanako.+
8 Kenako anapanga beseni losambira lamkuwa+ ndi choikapo chake chamkuwa. Popanga zimenezi anagwiritsa ntchito akalirole* a akazi otumikira, amene anali kutumikira mwadongosolo pachipata cha chihema chokumanako.+