Genesis 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kuchokera m’dzikoli analowera ku Asuri+ kumene anamanga Nineve,+ Rehoboti-iri, Kala, Yona 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Nyamuka upite kumzinda waukulu wa Nineve.+ Kumeneko ukadzudzule anthu a mumzindawo ndi kuwauza kuti ine ndaona zoipa zimene akuchita.”+ Nahumu 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Uwu ndi uthenga wokhudza Nineve:+ Buku la masomphenya a Nahumu wa ku Elikosi: Zefaniya 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Iye adzatambasulira dzanja lake kumpoto ndipo adzawononga Asuri.+ Adzachititsa Nineve kukhala bwinja,+ kukhala dziko lopanda madzi ngati chipululu.
2 “Nyamuka upite kumzinda waukulu wa Nineve.+ Kumeneko ukadzudzule anthu a mumzindawo ndi kuwauza kuti ine ndaona zoipa zimene akuchita.”+
13 “Iye adzatambasulira dzanja lake kumpoto ndipo adzawononga Asuri.+ Adzachititsa Nineve kukhala bwinja,+ kukhala dziko lopanda madzi ngati chipululu.