Genesis 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chotero Yehova anati: “Kudandaula kokhumudwa chifukwa cha Sodomu ndi Gomora+ kwamveka kwambiri, ndipo tchimo lawo n’lalikulu kwambiri.+ Yakobo 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamverani! Malipiro a anthu amene anagwira ntchito+ yokolola m’minda yanu, amene inu simunapereke,+ akufuula ndipo kufuula kwa okololawo kofuna thandizo+ kwafika m’makutu+ a Yehova wa makamu. Chivumbulutso 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti machimo ake aunjikana mpaka kumwamba,+ ndipo Mulungu wakumbukira+ zochita zake zopanda chilungamo.
20 Chotero Yehova anati: “Kudandaula kokhumudwa chifukwa cha Sodomu ndi Gomora+ kwamveka kwambiri, ndipo tchimo lawo n’lalikulu kwambiri.+
4 Tamverani! Malipiro a anthu amene anagwira ntchito+ yokolola m’minda yanu, amene inu simunapereke,+ akufuula ndipo kufuula kwa okololawo kofuna thandizo+ kwafika m’makutu+ a Yehova wa makamu.
5 Pakuti machimo ake aunjikana mpaka kumwamba,+ ndipo Mulungu wakumbukira+ zochita zake zopanda chilungamo.