Yesaya 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anapitiriza kunena kuti: “Pita ukauze anthu awa kuti, ‘Imvani mobwerezabwereza anthu inu, koma musamvetsetse. Onani mobwerezabwereza, koma musazindikire chilichonse.’+ Yesaya 42:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Inu ogontha imvani. Inu akhungu yang’anani kuti muone.+
9 Iye anapitiriza kunena kuti: “Pita ukauze anthu awa kuti, ‘Imvani mobwerezabwereza anthu inu, koma musamvetsetse. Onani mobwerezabwereza, koma musazindikire chilichonse.’+