Yesaya 44:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndani ali ngati ine?+ Ayankhe molimba mtima kuti apereke umboni wake kwa ine.+ Monga momwe ine ndachitira kuyambira nthawi imene ndinakhazikitsa anthu akalekale,+ iwo anene zinthu zimene zichitike posachedwa ndi zimene zidzachitike m’tsogolo. Yesaya 46:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ine ndi amene ndimanena za mapeto kuyambira pa chiyambi.+ Kuyambira kalekale, ndimanena za zinthu zimene sizinachitike.+ Ine ndiye amene ndimanena kuti, ‘Zolingalira zanga zidzachitikadi,+ ndipo ndidzachita chilichonse chimene ndikufuna.’+
7 Ndani ali ngati ine?+ Ayankhe molimba mtima kuti apereke umboni wake kwa ine.+ Monga momwe ine ndachitira kuyambira nthawi imene ndinakhazikitsa anthu akalekale,+ iwo anene zinthu zimene zichitike posachedwa ndi zimene zidzachitike m’tsogolo.
10 Ine ndi amene ndimanena za mapeto kuyambira pa chiyambi.+ Kuyambira kalekale, ndimanena za zinthu zimene sizinachitike.+ Ine ndiye amene ndimanena kuti, ‘Zolingalira zanga zidzachitikadi,+ ndipo ndidzachita chilichonse chimene ndikufuna.’+