Salimo 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mawu a pakamwa panga ndi kusinkhasinkha kwa mtima wanga,+Zikukondweretseni, inu Yehova, Thanthwe langa+ ndi Wondiwombola.+ Yesaya 44:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Yehova, Mfumu ya Isiraeli,+ Womuwombola iye,+ Yehova wa makamu, wanena kuti: ‘Ine ndine woyamba ndi womaliza,+ ndipo palibenso Mulungu kupatulapo ine.+ Yesaya 63:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Inutu ndinu Atate wathu.+ Ngakhale kuti Abulahamu sanatidziwe ndipo Isiraeli sanatizindikire, inuyo Yehova ndinu Atate wathu. Dzina lanu ndinu Wotiwombola wakalekale.+
14 Mawu a pakamwa panga ndi kusinkhasinkha kwa mtima wanga,+Zikukondweretseni, inu Yehova, Thanthwe langa+ ndi Wondiwombola.+
6 “Yehova, Mfumu ya Isiraeli,+ Womuwombola iye,+ Yehova wa makamu, wanena kuti: ‘Ine ndine woyamba ndi womaliza,+ ndipo palibenso Mulungu kupatulapo ine.+
16 Inutu ndinu Atate wathu.+ Ngakhale kuti Abulahamu sanatidziwe ndipo Isiraeli sanatizindikire, inuyo Yehova ndinu Atate wathu. Dzina lanu ndinu Wotiwombola wakalekale.+