4 momwemonso mfumu ya Asuri idzagwira gulu la anthu ku Iguputo+ ndi ku Itiyopiya n’kupita nawo ku ukapolo kudziko lina, anyamata ndi nkhalamba, ali opanda zovala ndi opanda nsapato, ndiponso matako awo ali pamtunda. Pamenepo, umaliseche wa Iguputo udzaonekera.+