Yesaya 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Babulo, amene ndi chokongoletsera maufumu,+ chinthu chokongola ndi chonyadira cha Akasidi,+ adzakhala ngati pamene Mulungu anagonjetsa Sodomu ndi Gomora.+ Yesaya 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 mudzanene mwambi uwu wotonza mfumu ya Babulo: “Uja ankagwiritsa ntchito anzakeyu wasiya ndithu! Wopondereza uja waleka ndithu!+ Chivumbulutso 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamphumi pake panalembedwa dzina lachinsinsi+ lakuti: “Babulo Wamkulu, mayi wa mahule+ ndi wa zonyansa za padziko lapansi.”+
19 Babulo, amene ndi chokongoletsera maufumu,+ chinthu chokongola ndi chonyadira cha Akasidi,+ adzakhala ngati pamene Mulungu anagonjetsa Sodomu ndi Gomora.+
4 mudzanene mwambi uwu wotonza mfumu ya Babulo: “Uja ankagwiritsa ntchito anzakeyu wasiya ndithu! Wopondereza uja waleka ndithu!+
5 Pamphumi pake panalembedwa dzina lachinsinsi+ lakuti: “Babulo Wamkulu, mayi wa mahule+ ndi wa zonyansa za padziko lapansi.”+