Ezekieli 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, kodi ndiwe wokonzeka kuweruza?+ Kodi uweruza mzinda umene uli ndi mlandu wa magaziwu+ ndi kuudziwitsa zonyansa zake zonse?+ Chivumbulutso 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti machimo ake aunjikana mpaka kumwamba,+ ndipo Mulungu wakumbukira+ zochita zake zopanda chilungamo.
2 “Iwe mwana wa munthu, kodi ndiwe wokonzeka kuweruza?+ Kodi uweruza mzinda umene uli ndi mlandu wa magaziwu+ ndi kuudziwitsa zonyansa zake zonse?+
5 Pakuti machimo ake aunjikana mpaka kumwamba,+ ndipo Mulungu wakumbukira+ zochita zake zopanda chilungamo.