Ezekieli 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Kodi ndiwe wokonzeka kuwaweruza? Kodi uwaweruza, iwe mwana wa munthu?+ Auze zinthu zonyansa zimene makolo awo anachita.+ Ezekieli 23:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Yehova anandiuzanso kuti: “Iwe mwana wa munthu, kodi uweruza+ Ohola ndi Oholiba+ ndi kuwauza zinthu zonyansa zimene achita?+
4 “Kodi ndiwe wokonzeka kuwaweruza? Kodi uwaweruza, iwe mwana wa munthu?+ Auze zinthu zonyansa zimene makolo awo anachita.+
36 Yehova anandiuzanso kuti: “Iwe mwana wa munthu, kodi uweruza+ Ohola ndi Oholiba+ ndi kuwauza zinthu zonyansa zimene achita?+