Ezekieli 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wamkulu dzina lake anali Ohola, wamng’ono anali Oholiba. Akazi amenewa anakhala anga+ ndipo anabereka ana aamuna ndi aakazi.+ Ohola akuimira Samariya+ ndipo Oholiba akuimira Yerusalemu.+
4 Wamkulu dzina lake anali Ohola, wamng’ono anali Oholiba. Akazi amenewa anakhala anga+ ndipo anabereka ana aamuna ndi aakazi.+ Ohola akuimira Samariya+ ndipo Oholiba akuimira Yerusalemu.+