Ezekieli 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “‘Unali kutenga ana ako aamuna ndi aakazi amene unandiberekera+ n’kumawapereka nsembe kwa mafano.+ Kodi zochita zako zauhulezo sizinakukwanire? Agalatiya 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsopano, Hagara ameneyu akutanthauza Sinai,+ phiri la ku Arabiya, ndipo masiku ano akufanana ndi Yerusalemu, pakuti ali mu ukapolo+ pamodzi ndi ana ake.
20 “‘Unali kutenga ana ako aamuna ndi aakazi amene unandiberekera+ n’kumawapereka nsembe kwa mafano.+ Kodi zochita zako zauhulezo sizinakukwanire?
25 Tsopano, Hagara ameneyu akutanthauza Sinai,+ phiri la ku Arabiya, ndipo masiku ano akufanana ndi Yerusalemu, pakuti ali mu ukapolo+ pamodzi ndi ana ake.