Salimo 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tandipempha,+ ndipo ndikupatsa mitundu ya anthu kukhala cholowa chako,+Ndikupatsa dziko lonse lapansi kukhala lako.+ Yesaya 54:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti iwe udzafutukukira mbali ya kudzanja lamanja ndi kumanzere, ndipo ana ako+ adzalanda ngakhale mitundu ya anthu.+ Iwo adzakhala m’mizinda imene inasiyidwa yabwinja.+
8 Tandipempha,+ ndipo ndikupatsa mitundu ya anthu kukhala cholowa chako,+Ndikupatsa dziko lonse lapansi kukhala lako.+
3 Pakuti iwe udzafutukukira mbali ya kudzanja lamanja ndi kumanzere, ndipo ana ako+ adzalanda ngakhale mitundu ya anthu.+ Iwo adzakhala m’mizinda imene inasiyidwa yabwinja.+