Salimo 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi mudzandiiwala kufikira liti, inu Yehova?+ Mpaka muyaya?+Mudzandibisira nkhope yanu kufikira liti?+ Maliro 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 N’chifukwa chiyani mwatiiwala kwamuyaya+ ndi kutisiya kwa masiku ambiri?+
13 Kodi mudzandiiwala kufikira liti, inu Yehova?+ Mpaka muyaya?+Mudzandibisira nkhope yanu kufikira liti?+