Chivumbulutso 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo malo opatulikawo anadzaza utsi chifukwa cha ulemerero wa Mulungu,+ ndiponso chifukwa cha mphamvu zake. Palibe amene anatha kulowa m’malo opatulikawo, mpaka miliri 7+ ya angelo 7 aja itatha.
8 Ndipo malo opatulikawo anadzaza utsi chifukwa cha ulemerero wa Mulungu,+ ndiponso chifukwa cha mphamvu zake. Palibe amene anatha kulowa m’malo opatulikawo, mpaka miliri 7+ ya angelo 7 aja itatha.