Ekisodo 40:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pamenepo mtambo+ unayamba kuphimba chihema chokumanako, ndipo ulemerero wa Yehova unadzaza m’chihemacho. 1 Mafumu 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa cha mtambowo, ansembewo+ analephera kupitiriza kutumikira,+ popeza ulemerero+ wa Yehova unadzaza nyumba ya Yehovayo.+ Yesaya 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa cha mawuwo, mafelemu a zitseko+ anayamba kunjenjemera ndipo pang’ono ndi pang’ono, m’nyumbamo munadzaza utsi.+ Ezekieli 44:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako ananditengera kutsogolo kwa Nyumba ija kudzera pachipata cha kumpoto kuti ndikaone zimene zinali kumeneko. Kumeneko ndinaona ulemerero wa Yehova utadzaza m’nyumba ya Yehova.+ Pamenepo ndinagwada n’kuwerama mpaka nkhope yanga pansi.+
34 Pamenepo mtambo+ unayamba kuphimba chihema chokumanako, ndipo ulemerero wa Yehova unadzaza m’chihemacho.
11 Chifukwa cha mtambowo, ansembewo+ analephera kupitiriza kutumikira,+ popeza ulemerero+ wa Yehova unadzaza nyumba ya Yehovayo.+
4 Chifukwa cha mawuwo, mafelemu a zitseko+ anayamba kunjenjemera ndipo pang’ono ndi pang’ono, m’nyumbamo munadzaza utsi.+
4 Kenako ananditengera kutsogolo kwa Nyumba ija kudzera pachipata cha kumpoto kuti ndikaone zimene zinali kumeneko. Kumeneko ndinaona ulemerero wa Yehova utadzaza m’nyumba ya Yehova.+ Pamenepo ndinagwada n’kuwerama mpaka nkhope yanga pansi.+