Salimo 74:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu Mulungu, kodi mdani adzakuchitirani mopanda ulemu kufikira liti?+Kodi mdani adzanyoza dzina lanu kwamuyaya?+ Salimo 94:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi anthu oipa adzakondwera kufikira liti?+Kodi adzakondwera kufikira liti, inu Yehova?+
10 Inu Mulungu, kodi mdani adzakuchitirani mopanda ulemu kufikira liti?+Kodi mdani adzanyoza dzina lanu kwamuyaya?+