Yeremiya 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo akuyesa kuchiritsa mwachinyengo+ kuwonongeka kwa anthu anga ponena kuti, ‘Kuli mtendere! Kuli mtendere!’ pamene kulibe mtendere.+ Ezekieli 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 kutanthauza aneneri a mu Isiraeli amene akulosera zokhudza Yerusalemu, amene akuona masomphenya onena za mzindawo kuti mudzakhala mtendere+ pamene simudzakhala mtendere,”’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+
14 Iwo akuyesa kuchiritsa mwachinyengo+ kuwonongeka kwa anthu anga ponena kuti, ‘Kuli mtendere! Kuli mtendere!’ pamene kulibe mtendere.+
16 kutanthauza aneneri a mu Isiraeli amene akulosera zokhudza Yerusalemu, amene akuona masomphenya onena za mzindawo kuti mudzakhala mtendere+ pamene simudzakhala mtendere,”’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+