Ezekieli 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Aneneri a mu Isiraeli adzakhala atawonongedwa. Aneneri amenewa ndi omwe akulosera zokhudza Yerusalemu nʼkumaona masomphenya oti mumzindawo muli mtendere, pamene mulibe mtendere,”’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:16 Nsanja ya Olonda,5/1/1997, ptsa. 8-9
16 Aneneri a mu Isiraeli adzakhala atawonongedwa. Aneneri amenewa ndi omwe akulosera zokhudza Yerusalemu nʼkumaona masomphenya oti mumzindawo muli mtendere, pamene mulibe mtendere,”’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.